Miyambo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wopusa amatulutsa mkwiyo wake wonse,+Koma wanzeru amakhala wodekha ndipo amalamulira mkwiyo wake.+
11 Munthu wopusa amatulutsa mkwiyo wake wonse,+Koma wanzeru amakhala wodekha ndipo amalamulira mkwiyo wake.+