-
Genesis 39:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Potifara anapitiriza kumukonda Yosefe ndipo anakhala mtumiki amene ankamudalira. Choncho anamusankha kuti akhale woyangʼanira nyumba yake komanso zinthu zonse zimene anali nazo.
-