Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 38:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndili ndi nkhawa komanso chisoni chachikulu.

      Ndikuyendayenda ndili wachisoni tsiku lonse.

  • Miyambo 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chinthu chimene umayembekezera chikalephereka, mtima umadwala.+

      Koma chomwe umalakalaka chikachitika, chimakhala ngati mtengo wa moyo.+

  • Miyambo 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa kuti nkhope izioneka yosangalala,

      Koma munthu sasangalala ngati mtima ukumupweteka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena