Miyambo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nzeru zimamanga nyumba ya* munthu,+Ndipo kuzindikira kumachititsa kuti ilimbe kwambiri. Miyambo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amatsegula pakamwa pake mwanzeru,+Ndipo lamulo la kukoma mtima lili* palilime lake.