Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa munthu wopusa, kuchita khalidwe lochititsa manyazi kuli ngati masewera,Koma munthu wozindikira amakhala ndi nzeru.+ Miyambo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene mkazi wachigololo amachita ndi izi: Iye amadya nʼkupukuta pakamwa pakeKenako amanena kuti, “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+
23 Kwa munthu wopusa, kuchita khalidwe lochititsa manyazi kuli ngati masewera,Koma munthu wozindikira amakhala ndi nzeru.+
20 Zimene mkazi wachigololo amachita ndi izi: Iye amadya nʼkupukuta pakamwa pakeKenako amanena kuti, “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+