Miyambo 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wodziwa zinthu amayamba waganiza asanalankhule,+Ndipo munthu wozindikira amapitiriza kukhala wodekha.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+
27 Munthu wodziwa zinthu amayamba waganiza asanalankhule,+Ndipo munthu wozindikira amapitiriza kukhala wodekha.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+