1 Mafumu 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kenako mfumuyo inauza Simeyi kuti: “Iweyo ukudziwa mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera pamutu pako zoipa zimene unachita.+ 1 Mafumu 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada kuti aphe Simeyi ndipo anamuphadi.+ Choncho ufumu unakhazikika mʼmanja mwa Solomo.+
44 Kenako mfumuyo inauza Simeyi kuti: “Iweyo ukudziwa mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera pamutu pako zoipa zimene unachita.+
46 Ndiyeno mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada kuti aphe Simeyi ndipo anamuphadi.+ Choncho ufumu unakhazikika mʼmanja mwa Solomo.+