Miyambo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwambi wamʼkamwa mwa anthu opusa+Uli ngati miyendo* ya munthu wolumala amene akuyenda motsimphina.