Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anatenga mikate 200, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo komanso anapha nkhosa 5. Anatenganso tirigu wokazinga wokwana miyezo 5 ya seya,* makeke 100 a mphesa zouma ndiponso makeke 200 a nkhuyu zouma nʼkuzikweza pa abulu.+

  • 1 Samueli 25:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kenako Davide analandira zimene Abigayeli anamubweretsera nʼkumuuza kuti: “Pita kunyumba kwako mwamtendere. Ndamvera mawu ako ndipo ndidzachita zimene wapempha.”

  • Miyambo 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mphatso ya munthu imamʼtsegulira njira,+

      Ndipo imamuthandiza kuti akafike kwa anthu olemekezeka.

  • Miyambo 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anthu ambiri amafuna kukondedwa ndi munthu wolemekezeka,*

      Ndipo aliyense ndi bwenzi la munthu wopereka mphatso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena