Miyambo 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu woyambitsa mavuto* amayambanitsa anthu,+Ndipo wonenera anzake zoipa amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
28 Munthu woyambitsa mavuto* amayambanitsa anthu,+Ndipo wonenera anzake zoipa amalekanitsa mabwenzi apamtima.+