Miyambo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanzeru amasangalatsa bambo ake,+Koma munthu wopusa amanyoza mayi ake.+