Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Kudzikweza kukafika manyazi amafikanso,+

      Koma anthu odzichepetsa ndi amene ali ndi nzeru.+

  • Danieli 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mʼmalomwake mwadzikweza pamaso pa Ambuye wakumwamba+ ndipo munalamula anthu kuti akubweretsereni ziwiya zamʼnyumba yake.+ Ndiyeno inuyo, nduna zanu, adzakazi anu ndi akazi anu ena mwamwera vinyo mʼziwiya zimenezi ndipo mwatamanda milungu yasiliva, yagolide, yakopa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala imene siona, kumva kapena kudziwa chilichonse.+ Koma Mulungu amene amakupatsani mpweya komanso amene ali ndi mphamvu zolamulira moyo wanu, simunamulemekeze.+

  • Danieli 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+

  • Machitidwe 12:21-23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pa tsiku lina lomwe anasankha, Herode anavala zovala zake zachifumu nʼkukhala pampando wake woweruzira milandu ndipo anayamba kulankhula ndi anthu. 22 Anthuwo atamva mawu ake anayamba kufuula kuti: “Amenewa ndi mawu a mulungu, osati a munthu!” 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova* anamudwalitsa, chifukwa sanalemekeze Mulungu. Ndipo anadyedwa ndi mphutsi nʼkufa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena