Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 19:25-27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Atafika* ku Yerusalemu kukakumana ndi mfumu, mfumuyo inamufunsa kuti: “Mefiboseti, nʼchifukwa chiyani sunapite nane?” 26 Iye anayankha kuti: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga+ ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu ndinamuuza kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu ndikwerepo kuti ndipite limodzi ndi mfumu,’ chifukwa ine mtumiki wanu ndine wolumala.+ 27 Koma mtumiki wangayo anakuuzani inu mbuyanga mfumu+ zinthu zabodza zokhudza ine mtumiki wanu. Komabe inu mbuyanga muli ngati mngelo wa Mulungu woona, choncho chitani zilizonse zomwe mukuona kuti nʼzabwino.

  • Miyambo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Usamafulumire kupititsa mlandu kukhoti,

      Chifukwa udzachita chiyani mnzako akadzapereka umboni wosonyeza kuti iweyo ndi wolakwa?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena