Miyambo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amasangalala ndi zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake abwino,*+Ndipo ntchito za manja ake zidzamupindulira. Miyambo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu adzadya zinthu zabwino kuchokera pa zipatso zapakamwa pake,+Koma anthu achinyengo amalakalaka kuchita zachiwawa.
14 Munthu amasangalala ndi zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake abwino,*+Ndipo ntchito za manja ake zidzamupindulira.
2 Munthu adzadya zinthu zabwino kuchokera pa zipatso zapakamwa pake,+Koma anthu achinyengo amalakalaka kuchita zachiwawa.