Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 104:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ochimwa adzachotsedwa padziko lapansi,

      Ndipo oipa sadzakhalaponso.+

      Moyo wanga utamande Yehova. Tamandani Ya!*

  • Miyambo 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+

      Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+

  • Mateyu 25:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Anthu amenewa adzachoka kupita kuchiwonongeko chosatha,*+ koma olungama kumoyo wosatha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena