Miyambo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Izi ndi zimene anthu ofuna kupeza phindu mwachinyengo amachita,Ndipo phindu limene apezalo lidzachotsa moyo wawo.+ Miyambo 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu akapeza cholowa mwadyera,Pamapeto pake Mulungu sadzamudalitsa.+
19 Izi ndi zimene anthu ofuna kupeza phindu mwachinyengo amachita,Ndipo phindu limene apezalo lidzachotsa moyo wawo.+