Yoswa 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukhale wolimba mtima kwambiri ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Uonetsetse kuti ukutsatira malamulo onse amene mtumiki wanga Mose anakulamula. Usapatukire kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ kuti uzichita zinthu mwanzeru kulikonse kumene ungapite.+ Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+
7 Ukhale wolimba mtima kwambiri ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Uonetsetse kuti ukutsatira malamulo onse amene mtumiki wanga Mose anakulamula. Usapatukire kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ kuti uzichita zinthu mwanzeru kulikonse kumene ungapite.+
9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+