Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Onani munthu wosalakwa,*Ndipo yangʼanitsitsani munthu wolungama,+Chifukwa tsogolo la munthu ameneyo lidzakhala lamtendere.+ Miyambo 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu owongoka mtima amapewa kuchita zinthu zoipa. Aliyense amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+ 1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+
37 Onani munthu wosalakwa,*Ndipo yangʼanitsitsani munthu wolungama,+Chifukwa tsogolo la munthu ameneyo lidzakhala lamtendere.+
17 Anthu owongoka mtima amapewa kuchita zinthu zoipa. Aliyense amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+
22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+