-
1 Samueli 25:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Nabala anawayankha kuti: “Kodi Davide ndi ndani, ndipo mwana wa Jese ndi ndani? Masiku ano atumiki ambiri akukonda kuthawa ambuye awo.+ 11 Ndiye zoona ine nditenge mkate wanga, madzi ndi nyama imene ndaphera antchito anga ometa ubweya wa nkhosa nʼkupereka kwa amuna amene sindikudziwa kumene achokera?”
-