Miyambo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira. Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya munthu wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere,+Ndipo dzudzula munthu womvetsa zinthu kuti awonjezere zimene akudziwa.+
9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.
25 Menya munthu wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere,+Ndipo dzudzula munthu womvetsa zinthu kuti awonjezere zimene akudziwa.+