Salimo 141:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, ikani mlonda pakamwa panga.Ikani woti azilondera patsogolo pa milomo yanga.+ Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Mlaliki 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale mʼmaganizo mwako,* usatemberere* mfumu+ ndipo usatemberere munthu wolemera kuchipinda kwako. Chifukwa mbalame* ikhoza kutenga mawu ako* kapena cholengedwa chokhala ndi mapiko chikhoza kukaulula zimene wanenazo.
19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
20 Ngakhale mʼmaganizo mwako,* usatemberere* mfumu+ ndipo usatemberere munthu wolemera kuchipinda kwako. Chifukwa mbalame* ikhoza kutenga mawu ako* kapena cholengedwa chokhala ndi mapiko chikhoza kukaulula zimene wanenazo.