Miyambo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wosangalala ndi munthu amene nthawi zonse amasamala zochita zake,*Koma amene amaumitsa mtima wake adzakumana ndi tsoka.+ Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu amene amaumitsa khosi lake* pambuyo podzudzulidwa mobwerezabwereza+Adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo sadzachira.+
14 Wosangalala ndi munthu amene nthawi zonse amasamala zochita zake,*Koma amene amaumitsa mtima wake adzakumana ndi tsoka.+
29 Munthu amene amaumitsa khosi lake* pambuyo podzudzulidwa mobwerezabwereza+Adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo sadzachira.+