Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Chifukwa milomo ya mkazi wamakhalidwe oipa* imakha uchi ngati chisa cha njuchi,+

      Ndipo mʼkamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+

  • Mlaliki 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiye ndinapeza izi: Mkazi amene ali ngati ukonde wosakira nyama, amene mtima wake uli ngati khoka, komanso amene manja ake ali ngati unyolo wakundende, ndi wowawa kwambiri kuposa imfa. Munthu amene amasangalatsa Mulungu woona adzamuthawa,+ koma wochimwa amagwidwa naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena