Salimo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”* Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”*
31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+