-
Afilipi 3:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma zinthu zimene zinali zaphindu kwa ine ndikuziona kuti ndi zopanda phindu* chifukwa cha Khristu.+ 8 Zoonadi, ndimaona kuti zinthu zonse nʼzosapindulitsa chifukwa chakuti ndinadziwa Khristu Yesu Ambuye wanga, chimene ndi chinthu chamtengo wapatali kwambiri. Chifukwa cha iye, ndinataya zinthu zonse ndipo ndimaziona ngati mulu wa zinyalala, kuti ndikhale pa ubwenzi weniweni ndi Khristu,
-