Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aliyense wanzeru aona zinthu zimenezi+Ndipo aganizira mofatsa zimene Yehova wachita posonyeza chikondi chake chokhulupirika.+
43 Aliyense wanzeru aona zinthu zimenezi+Ndipo aganizira mofatsa zimene Yehova wachita posonyeza chikondi chake chokhulupirika.+