Yobu 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi ndinayamba ndasangalalapo chifukwa cha kuwonongedwa kwa mdani wanga,+Kapena kunyadira chifukwa chakuti zoipa zamuchitikira? Miyambo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wonyoza munthu wosauka amanyoza amene anamupanga.+Ndipo amene amasangalala ndi tsoka la wina sadzalephera kulangidwa.+ Miyambo 25:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati mdani wako* ali ndi njala, umʼpatse chakudya.Ngati ali ndi ludzu, umʼpatse madzi akumwa,+22 Ukachita zimenezi ndiye kuti ukumuunjikira makala amoto pamutu pake,*+Ndipo Yehova adzakupatsa mphoto.
29 Kodi ndinayamba ndasangalalapo chifukwa cha kuwonongedwa kwa mdani wanga,+Kapena kunyadira chifukwa chakuti zoipa zamuchitikira?
5 Wonyoza munthu wosauka amanyoza amene anamupanga.+Ndipo amene amasangalala ndi tsoka la wina sadzalephera kulangidwa.+
21 Ngati mdani wako* ali ndi njala, umʼpatse chakudya.Ngati ali ndi ludzu, umʼpatse madzi akumwa,+22 Ukachita zimenezi ndiye kuti ukumuunjikira makala amoto pamutu pake,*+Ndipo Yehova adzakupatsa mphoto.