Miyambo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense wonena kuti munthu woipa alibe mlandu ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi wolakwa,+Onsewa ndi onyansa kwa Yehova.
15 Aliyense wonena kuti munthu woipa alibe mlandu ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi wolakwa,+Onsewa ndi onyansa kwa Yehova.