Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo. 1 Timoteyo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uziwadzudzula+ pamaso pa onse kuti ena onsewo akhale ndi mantha.*
17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo.
20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uziwadzudzula+ pamaso pa onse kuti ena onsewo akhale ndi mantha.*