-
Mlaliki 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma, kaya adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.
-