Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzakhalitsidwa chete* chifukwa cha kusadziwa. Popeza iwo akana kundidziwa,+Inenso ndidzawakana kuti asamanditumikire ngati wansembe wanga.Komanso chifukwa chakuti iwo aiwala lamulo* la ine Mulungu wawo,+Inenso ndidzaiwala ana awo.
6 Anthu anga adzakhalitsidwa chete* chifukwa cha kusadziwa. Popeza iwo akana kundidziwa,+Inenso ndidzawakana kuti asamanditumikire ngati wansembe wanga.Komanso chifukwa chakuti iwo aiwala lamulo* la ine Mulungu wawo,+Inenso ndidzaiwala ana awo.