Miyambo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene amasunga lamulo amasunga moyo wake.+Amene amachita zinthu mosasamala adzafa.+ Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, mudzakhala osangalala mukamazichita.+ Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.
25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.