Mlaliki 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Usamapupulume kulankhula kapena kulola kuti mtima wako ufulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba koma iwe uli padziko lapansi. Nʼchifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+
2 Usamapupulume kulankhula kapena kulola kuti mtima wako ufulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba koma iwe uli padziko lapansi. Nʼchifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+