Miyambo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zolankhula za munthu wopusa zimayambitsa mikangano,+Ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+ Miyambo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu amalemekezeka akapewa mkangano,+Koma aliyense wopusa amafulumira kuyambitsa mkangano.+