Mateyu 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mutipatse chakudya chimene* tikufunikira lero.+ 1 Timoteyo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ngati tili ndi chakudya, zovala ndi pogona, tizikhala okhutira ndi zinthu zimenezi.+