Deuteronomo 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mukapanda kulonjeza, simudzachimwa.+ Miyambo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Umakhala msampha munthu akathamangira kufuula kuti, “Nʼzoyera!”+ Koma pambuyo polonjeza nʼkuyamba kuganiziranso bwino zimene walonjezazo.+
25 Umakhala msampha munthu akathamangira kufuula kuti, “Nʼzoyera!”+ Koma pambuyo polonjeza nʼkuyamba kuganiziranso bwino zimene walonjezazo.+