Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chifukwa akadzamwalira sadzatenga china chilichonse.+

      Ulemerero wake sadzapita nawo limodzi.+

  • Luka 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+

  • 1 Timoteyo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pajatu sitinabwere ndi kanthu mʼdziko ndipo sitingachokemo ndi kanthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena