-
Mlaliki 3:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndazindikira kuti palibe chabwino kuposa kuti iwo asangalale ndiponso kuti azichita zabwino pamene ali ndi moyo,+ 13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa nʼkumasangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa cha ntchito yake yonse imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+
-