-
Yesaya 5:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka mʼmamawa kwambiri kuti amwe mowa,+
Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.
12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe,
Maseche ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.
Koma saganizira zochita za Yehova,
Ndipo saona ntchito ya manja ake.
-