Miyambo 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzikuza kumangoyambitsa mikangano basi,+Koma anthu amene amapempha malangizo* amakhala ndi nzeru.+ Yakobo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo cha aneneri amene analankhula mʼdzina la Yehova.*+ 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
10 Kudzikuza kumangoyambitsa mikangano basi,+Koma anthu amene amapempha malangizo* amakhala ndi nzeru.+
10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo cha aneneri amene analankhula mʼdzina la Yehova.*+
5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+