Miyambo 4:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upeze nzeru, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa zimene ndimakuuza. 6 Nzeruzo usazisiye ndipo zidzakuteteza. Uzikonde ndipo zidzakuteteza.
5 Upeze nzeru, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa zimene ndimakuuza. 6 Nzeruzo usazisiye ndipo zidzakuteteza. Uzikonde ndipo zidzakuteteza.