Yakobo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pali aliyense amene akukumana ndi mavuto pakati panu? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali aliyense amene akusangalala? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+
13 Kodi pali aliyense amene akukumana ndi mavuto pakati panu? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali aliyense amene akusangalala? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+