Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+ 1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, ipha ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi wa ku Edomu+ anapha ansembewo. Tsiku limenelo anapha amuna 85 ovala efodi wa nsalu.+
8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+
18 Ndiyeno mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, ipha ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi wa ku Edomu+ anapha ansembewo. Tsiku limenelo anapha amuna 85 ovala efodi wa nsalu.+