Miyambo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wanzeru amagonjetsa* mzinda wa anthu amphamvu,Ndipo amawononga mpanda wolimba umene amadalira.+ Miyambo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru ndi wamphamvu,+Ndipo akakhala wodziwa zinthu amawonjezera mphamvu zake.
22 Munthu wanzeru amagonjetsa* mzinda wa anthu amphamvu,Ndipo amawononga mpanda wolimba umene amadalira.+