Mlaliki 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Mulungu woona adzaweruza olungama ndi oipa omwe+ chifukwa pali nthawi yoyenera yoti chinthu chilichonse chichitike.”
17 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Mulungu woona adzaweruza olungama ndi oipa omwe+ chifukwa pali nthawi yoyenera yoti chinthu chilichonse chichitike.”