Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 3:17-19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngakhale oipa asiya kuvutika kumandako,

      Ndipo kumeneko anthu ofooka, akupuma.+

      18 Kumeneko akaidi onse ali pa mtendere.

      Iwo samvanso mawu a munthu wowakakamiza kugwira ntchito.

      19 Anthu onyozeka ndi olemekezeka amakhala chimodzimodzi kumeneko,+

      Ndipo kapolo amamasuka kwa mbuye wake.

  • Mlaliki 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Zimene zimachitikira opusa inenso zidzandichitikira.”+ Ndiye ndinapindula chiyani chifukwa chokhala wanzeru kwambiri? Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Izinso nʼzachabechabe.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena