Yobu 7:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mofanana ndi mtambo umene umazimiririka nʼkutha,Munthu amene wapita ku Manda,* sabwerera.+ 10 Iye sadzabwereranso kunyumba yake,Ndipo anthu a pamalo ake sadzamukumbukiranso.+ Mlaliki 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa munthu wanzeru komanso munthu wopusa,+ onsewa sadzakumbukiridwa mpaka kalekale. Mʼmasiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalika. Ndipo kodi wanzeru adzafa bwanji? Adzafa mofanana ndi wopusa.+
9 Mofanana ndi mtambo umene umazimiririka nʼkutha,Munthu amene wapita ku Manda,* sabwerera.+ 10 Iye sadzabwereranso kunyumba yake,Ndipo anthu a pamalo ake sadzamukumbukiranso.+
16 Chifukwa munthu wanzeru komanso munthu wopusa,+ onsewa sadzakumbukiridwa mpaka kalekale. Mʼmasiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalika. Ndipo kodi wanzeru adzafa bwanji? Adzafa mofanana ndi wopusa.+