Danieli 10:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Masiku amenewo, ineyo Danieli, ndinakhala ndikulira+ kwa milungu itatu yathunthu. 3 Sindinadye chakudya chokoma, sindinadye nyama kapena kumwa vinyo ndipo sindinadzole mafuta aliwonse kwa milungu itatu yathunthu.
2 Masiku amenewo, ineyo Danieli, ndinakhala ndikulira+ kwa milungu itatu yathunthu. 3 Sindinadye chakudya chokoma, sindinadye nyama kapena kumwa vinyo ndipo sindinadzole mafuta aliwonse kwa milungu itatu yathunthu.