2 Samueli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ahitofeli ataona kuti malangizo ake sanatsatiridwe, anakwera bulu nʼkupita kunyumba yake mʼtauni yakwawo.+ Kenako anapereka malangizo kwa anthu amʼbanja lake+ ndipo atatero anadzimangirira.+ Iye anafa ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake.
23 Ahitofeli ataona kuti malangizo ake sanatsatiridwe, anakwera bulu nʼkupita kunyumba yake mʼtauni yakwawo.+ Kenako anapereka malangizo kwa anthu amʼbanja lake+ ndipo atatero anadzimangirira.+ Iye anafa ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake.