-
Salimo 148:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tamandani Yehova, inu okhala padziko lapansi,
Inu zamoyo zikuluzikulu zamʼnyanja komanso inu nonse madzi akuya,
-
Luka 2:48, 49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Makolo akewo atamuona anadabwa kwambiri, ndipo mayi ake anamufunsa kuti: “Mwanawe, nʼchifukwa chiyani wativutitsa chonchi? Ine ndi bambo akowa tinali ndi nkhawa kwambiri ndipo timakufunafuna.” 49 Koma iye anawayankha kuti: “Mumandifunafuna chifukwa chiyani? Kodi simumadziwa kuti ndiyenera kupezeka mʼnyumba ya Atate wanga?”+
-
-
-